Get Complete Song Lyrics

Sholigah - Afa Ndi Mtima lyrics

Hook

Ndimomwe ndimaimbila fans imandifila...

Haaa! Fans imandifila Nde...

Ndimomwe ndimavalira mphasha ndimaisata,

Dollar ndimazisaka, zina ndimazimwaza.

Olimbana ndi ine, afa ndi mtima.

Ofuna kupanga za ine, afa ndi mtima.

Ofuna kugwetsa ine adah, afa ndi mtima.

Afune asafuna koma afa ndi mtima...



Vers1



Anawa amaimba koma mmmh adah mu yao.

Amatha kumenya single ndikuposa album yao.

Pano ndili pa mwamba ngati

Pa Zoba wina Dazi.

Ngati muli otentha ndi otcheni (ocean) ngati Madzi.

Ndili sick, Kwambili... Nthenda yake Yoopysa”

Andipeza ndi TB ndafanana ndi Josua”

Nyimbo zanga ndi Psquare zinafika Popita (paul, peter).

Olimbana ndi Sholigah akusowa Chochita.

Ndili ngati PC naneso ndimazi Sata“

Chifukwa ndinatchuka akazi amandiSaka.

Palibe amandidya koma ine ndiotopa.

Ngati sumandidziwa phwanga iweso ndi Zoba.

Ambiliwa samatha nde palibe angandigwetse Man.

Ndimazifila ngati thukuta la yesu mu Getsemani“

Ndinu makwacha adah,, ndine Pound.

Zima style ndizambili ndi Masintha, Ground.



(Hook)



Vers2

Zaine amachonga Nike koma ndine All star.

Show ya makape sindipezeka pa Poster“

Ukape sindimatha, mboni yanga ndi Yung-z.

Creo amadanda coz ndimakonda Nazi.

Ndili pamwamba zedi ndizatsikapo ndi patachute.

Ndimatchena ndili bare olo nditavala suit.

Akazi ofuna ine amangopanya ma CV.

Ngati sumandidziwa mphwawi kwanu kulibe TV.

Fans imandifila, ndimathokoza Jesus.

Ndima disser mafana opusa ndikukhalitsa ziii basi.

Sholigah ndi mazoba savana (savanna) ngati bawa.

Pa gulu lamazoba nde sholigah amatha.

Zokuti ndine chiphe aliyese amadziwa,

Amene amakuposayo kwaine amadiwa.

Ndili ngati Zimbabwe naneso ndili pa Map.

Hip-hop ikhale barcreys

Bwezi ndikungotenga ma cup



(Hook)



Vers3

Ma mcees achulukawa ndi

Nde sholigah kuimba bwinoku

Chifukwa kuimba bwinoku kwaiye ndi

Nde zothoka zopusa mafana pumulani.

Ndine chigawenga ndinapachika nkhawa zanga.

Ndimapha aliyese kaya anzanga.

Ndilibe chibale ndili ngati faith.

Ndimakhala ndabanda nde ndikamaika vers.



Ndimatha chilichonse kupatula china chake. chimaenda usiku

Ndaiwala ndina lake

Ambiliwa ndi ma MIN simomwe amandiOPERA.

Zoti amandiposa sizingamveke or atakasiya pa air *2.



Hook






0 comments:

Post a Comment

Sholigah - Afa Ndi Mtima lyrics